Umamva Bwanji-Maskal无损flac下载mp3下载
Umamva Bwanji-Maskal 在线试听歌词免费下载
ukakhala ndi ine baby
nthumazi imandigwira baby
nthawi zonse ukatalikira
ndimagwidwa ndi maganizo
ndimasowa chithandizo
ndidziwa bwanji za mtima mwako
poti udziwa wekha!
ukakhala ndi anzako
umawawuza chani za ine
umaganiza chani baby
ndiwuze ndidziwe
mu mtima mwako ndi ine
popeza unandidziwa
utapasidwanso mwayi osankha
ungasankhe ine!
ndiwuze ndidziwe eee
nkuthekatu zili bwino
unemkumati zili bwino
pali zambiri ndimafuna nditadziwa
umaganiza chani baby
ndiwuze ndi dziwe
Umamva Bwanji-Maskal歌曲下载
| 歌曲 | 歌手 | 专辑 | 时长 | 歌曲下载 |
|---|---|---|---|---|
| Umamva Bwanji | Maskal | Umunthu | 03:22 |
|
Umamva Bwanji-Maskal热门评论
Umamva Bwanji-Maskal 同专辑其他歌曲
- Linga Langa-Maskal
- Sindinazolowere-Maskal
- Zili Ndi Iwe-Maskal
- Umpeze Wina-Maskal
- Wampeza-Maskal
- Kudzagwa Mvula-Maskal
- Usatope-Maskal
- Akanapanda Kudziwa-Maskal
- Chikondi-Maskal